Intro
It's black volt
Kasungu music
Verse 1
Bebi yanga bwela pafupi
Kumwetulila kwako kumandipatsa moyo
Wukamayenda mtima wanga wumagunda
Kutali kutali ndimakusowa
Ndikufuna wuzikhala nane ngati wanga
Ndalota za iwe usiku wonse
Maso ako kuwala ngati nyenyezi
Ndipo dzina lako pamilomo panga osachoka
Black volt akulilila pachikondi chako
Hook
Kutali kutali
Enawa ali kutali
Bwela kwa ine
Wukakhale panyumba
Sindikufuna wina chifukwa iwo
Ali kutali
Kutali kutali
Ndikayenda ine ndimadziva
Ndili kutali
Verse 2
Tiye tivine mpaka m'banda kucha
Manja anga ine pamanja ako
Palibe nkhawa iweyo ndiwanga
Anthu anene zomwe akufuna
Koma ine ndi iwe ndife awili
Ndalama zimatha koma chikondi sichimatha
Ndili ndimawu mtima wanga
Tengani mtimawu ngati mphatso yachikondi
Iyi ndinyimbo yanga ndiyako yachikondi
Hook
Kutali kutali
Enawa ali kutali
Bwera kwa ine
Wukakhale panyumba
Sindikufuna wina chifukwa iwo
Ali kutali
Kutali kutali
Ndikayenda ine ndimadziva
Ndili kutali
Outro
Kutali kutali....bwera kwa ine
Ukakhala pafupi....ndimava mtendele
Pena ndimakusowa ....ukakhala kutali
Phokoso ndichikondi .....zili kutali
Ine kutumiza uthenga.....koma uli kutali
Black volt kubalalika iwe ...ukhala kutali
Hook
Kutali kutali
Enawa ali kutali
Bwela kwa ine
Wukakhale panyumba
Sindikufuna wina chifukwa iwo
Ali kutali
Kutali kutali
Ndikayenda ine ndimadziva
Ndili kutali
It's Black volt