This is Captain Nyakamera
Verse 1
Odi! Odi apapokha mkambe chilungamo//
Ndimakukonda tiye kwathu ku Chilomo//
Ukukaika? bwanji ukupinda Mulomo?//
Iwe ndi ine tizathera Mchikondi momo//
Verse 2
Suntha Mkazi wanga Mery Suntha//
Ndikukonda za hard eya! Ndikukonda za Luntha//
Sindizakusiya, Babe zaku Fela//
Tizayendabe awili bola kundimvera//
Chorus.
Paiwe ndatola Joker!
Joker, Joker, Joker!
Ansanje onse akhale!
Khale, Khale, Khale!
Tizakhala limodzi!
Kulikonse pamodzi!
Chikondi choyera chokongola ngati Madzi!!!
Verse 3
Mvetsela Mkazi!//
Ndimakukonda kwabasi//
Chikondi chowala ngati nkhope ya Dorcas!//
Chikondi chama Las//
Chopanda Jealous//
Basi, tipemphere kwa Jesus//
Kuti tizingokhalelabe limodzi//
Verse 4
Nyengo pena zimatha kusibtha//
Zinthu kuyamba kuyenda mwapendapenda//
Koma mchimodzi chomwe kwaiwe ndikupempha//
Osazandisiya pitiliza kukhala wanga//
Iwe Mary Chitsotso //
Tiye ndikonde Mwaluso//
Ndikuchotsa Kwa Mgabu, ukakhale kwathu kwa Nthukuso//