Moyowu uli ndi zokhumba...Zina zaku thupi Zina zaku uzimu...ukakhala ndi mzeru ukondweletsa mzimu.. thupi limalema imfa imakula mphamvu. Usakopeke ndizodutsa ugwire YESU.. Mwana wa Mulungu mfumu ya mafumu..ukapusa usochera kumasano utsikira.
HOOK "Mwana wanga samala samala...YESU akuyitana vomera vomera.. mawu a Mulungu mtima mwako kopela kopela.. Mzimu wa Ambuye mwaiwe agonera gonera (REPEAT HOOK)
Ine Jonathan Nkhonjera nditumikira..ndithamanga mkagwire mbendera..ndikhumbo langa mbweze osochera..pakutero Ambuye amwemwetera...
HOOK2 "Thamanga Mwana wanga thamanga..YESU akuyitana thamanga..mawu a Mulungu mtima mwako kopela kopela.. mzimu wa Ambuye mwaiwe agonera gonera