( clear Pronunciation )
[Intro]
Ah yeah... HUMBLE SLIM3 MW
Ndikuopa... ndikuopa kukondaso
[Verse 1]
Ndinakukondani kwambiri, ndinapereka mtima wanga wonse
Koma anasewera nawo ngati mpira, anasiya ndi mabala okha
Tsopano ndakumana nawe, iwe ndiwe wosiyana kwambiri
Koma mtima wanga ukunjenjemera, ukuopa kuvulalanso
[Chorus]
Ndikuopa kukondaso, ndikuopa kupwetekanso
Koma maso ako akunena kuti undikhulupirire
Ndikuopa kukondaso, ndikuopa kusweledwa mtima
Koma ngati uli weniweni, tiyeseni limodzi mwana
[Verse 2]
Ninataka kukuambia ninakupenda, lakini naogopa tena
Upendo wa kwanza uliniuma, moyo wangu unaumia
Wewe unanichekesha, unanifanya nisahau zam upani
Naomba usiwe kama yeye, uwe tofauti na yeye
[Chorus]
Ndikuopa kukondaso, ndikuopa kupwetekanso
Koma maso ako akunena kuti undikhulupirire
Ndikuopa kukondaso, ndikuopa kusweledwa mtima
Koma ngati uli weniweni, tiyeseni limodzi mwana
[Outro]
Ndikuopa kukondaso... lakini ninakupenda wewe up