Intro Za, za, zambuye izi, mtima kuwawa kamaganizila zonadi munapita ngati boza agogo anga inu!!!!
Vers pa 6 apr 2026 siku ili sindingali iwale
10 am ndili mu sika ndinalandila call agogo kuno atisiya
Ndinayang'ana pa phone paka 2 minutes
Kenako ndinapanga reply agogo ake ati?
Kenako ndinava agogo ako ayiye ndina sweka tima ndinafusa serious? Ndipo anati eya limbatima phix ndinabalalika kwambili ndinanyamuka kupita padeni ndinapeza ayinga anga akulila akuti ayiye tazukani chizukulu chanu chabwela muchione akukuwa!!! Ndinakhesa msozi kuwadandaula agogowanga ine kumati zonadi mwandisiya ndekha kulowa nyumba kumuona bizzo tose misozi ikungosika akundiuza ayiye apitadi ngati boza (crying!!!!) Why so soon koma? Akundiuza muthu amene tikakanganila bele tili ana uja sitizamuonaso!!! Sitikaziwakuti zizakhala chochi,
Sitikaziwa kuti mungapite chocho,
Thenda yoyamba sunday 4 pm pamene limafika monday 8 am mwatisiya ambuye munalolelanji kutidulila tengowu
Unalindimasamba ambili ife ndipamene tima bisala zuwa likama otcha ndikuziwa munawakondesesa koma mukanatikomela mtima ayiye ndimakukondani ndikukusowani muve kumene muliko ndikukusowani ndinu mayi oposa mai ose
Outro mulungu akupaseni korona