intro
uh-huh eh eh eh
it's black volt
(female voice)
kasungu music
hook
zakomela eni dziko
zakomela eni
munthu obwela sakufunidwa
koma ngati ndikusawukaku
ayi Malawi tazuzika
zakomela eni dziko
zakomela eni dziko
tikunena South Africa
verse 1
poyamba munali abwezi
lelo chasintha ndichani?
kapena mwina ndi ndale?
koma ngati ndindale ayi mwalanga
ndipo nditsankho lanuli muzisowa abwezi
dziko likakhala lankhaza ,chuma chimayamba kusowa
chatsala kuno shop right muzachose
ife timapeza kothawila ulova
tawonani mwatisiya pa zero
hook
zakomela eni dziko
zakomela eni dziko
munthu obwela sakufunidwa
koma ngati ndikusawukaku
ayi Malawi tazuzika
verse 2
amalawi tisadandawule
ena tili ndi moyo tiyamike mulungu
ena tilibe poyambila tidkile ku boma
tithokoze anthu amene atengapo gawo kuti Amalawi abweleko kujoni
mkazi onyada amafa ndiwumbeta
south Africa yanyada mawa amalawi azawafuna
chifukwa dziko ndi anthu obwela
ndimathokoza mulungu pondiponya kumalawi
dziko lawufulu ,dziko la mtendele
zikomo ambuye ,zikomo ambuye!!
outro
zakomela eni..... dziko
anthu obwela..... sakufunidwa
Zimbabwe....siyikufunidwa
Malawi..... siyikufunidwa
Nigeria.... siyikufunidwa
dziko Lilonse ku south Africa
siyikufunidwa
hook
zakomela eni dziko
zakomela eni dziko
anthu obwela sakufunidwa
koma ngati ndikusawukaku
ayi Malawi tazuzika
zakomela eni dziko
tikunena South Africa