{intro}
Wachiyao lucky wadzaso kachikena!
Ndine !, wamunamiyasi ghetto.
{Verse1}
Pano ine mama ndapata
Ndati ine ndapeza
Nkazi osamala wakhalidwe lowala uyu obaba ine ndati ndapata
Mwayiyeyu muli lavu mbambande,
Ndipo zachikondi chake mbamba palibe angalande
Mwaliyu timavana ndipo timakhalana,
Palibe kucheuka mbuyo nditapeza wanga mtendere
Enanu mukagwere mulibe chikondi munkangofuna basi mundibele
Apano mundilila ndipo ndati mukhaula popeza
Man frank apezano chimakina ndipo tikuvana and kukhalana mwayiyeyu muli zonse ndimomwe ndikupeza pano
{Chorus}
Mtendereeee
Ndati mtendere, mtendere wanga umu ndimomwe ndipata ine mama mtendere
Mwayiyeyu!! (uuuu!) mwayiyeyu mama muli
Chimwemwe
{Verse2}
Inu osanama ndimachedwa
Ndipo osati masewera
Chikondi nalinacho kwaiwo ndimagawa
Koma zosayenda poti ankangondiyuza
Amangofuna ndalama zanga osati chikondi (shaaaa!)
Ndinali chipatala mwachidule matenite omangobwera kwaine eti akavutika haaa
Nawo adona game over apa aviyeta timati wapanga fiyuuu! (wauluka)
Munkadziva vuto ukwini kaya mwina, koma izo kwanu konko apanotu ndapeza nkazi odziwa ponditobwanya
Nkazi osamala inu nkazi ochengeta
Odziwa chomwe ali ndikumandipatsaso
Chorus}
Mtendereeee
Ndati mtendere, mtendere wanga umu ndimomwe ndipata ine mama mtendere
Mwayiyeyu!! (uuuu!) mwayiyeyu mama muli
Chimwemwe
{Bridge}
Apa ndipo ndapata osanama frank wakhwana
Zoti kuliso chikondi chonchi pena ngati ndikulota
Mtendere wamumtima ndaupeza ndingoenera kukuwa kuti
Pre-Chorus}
Mtendereeee!!!
Ndati mtendere!!, mtendere wanga umu ndimomwe ndipata ine mama mtendere!!
Mwayiyeyu!! (uuuu!) mwayiyeyu mama!!! muli,
(Chimwemwe)
Mwaiweyo Mami (Mtendere)
Ndimomwe ndiona!!!,
Chimwemwe
{Outro}
Ndilinawe mpaka kareeeee
Nabola osasitha dear,
Iwe ndine mpaka paguwaa