###**Versao Tiye kwathu akakuone mam ndi dadi
___________________
King Dropa
Kodi nanwaliwe unachita chobadwa kapena mwina ungogwa kumwamba maonekedwe ako mavalidwe ako ngakhaleso kayendedwe kako zikundibalalitsa mutima
###**Versao " Tiye kwathu akakuone mam ndi dadi
____________________
Ndikukhulupilila kati mama ndi dadi akakondwela napezela mpongozi Chonde namwali tandilole mwamsanga koti tiuze anthu afulule thobwa khuku ziphedwe.
Dropas Beat