introduction (chikwiri yamaceleb)
(verse 1)
ndine innocent Hayward oo! iyeh!
chikwiri mudzi wachisanzo
anthu ake samalowa mjango
mboni ndi achina chisanzo
iliyonse ndi Hustl
kaya yoweta mikango
Jerald pala moto
muuze innock chikwiri ayake moto
(verse 2)
yachina Patrick Francisco
chikwiri ayake moto
azungu abwele konko
show sitipanga ndi azigogo
akamabwera timawawuza bwelelani konko
ana timawawuza kuno Toto
mudzi wathu sitilola nkhondo
sitipqngilamo chipako chikwiri mofaya
(verse 3)
yoh! yoh! Lawrence Timothy
chikwiri mayi koto
chikondi mayikolo
ife tinabadwila muno
ndipo tizafela kuno
ndikulephela kusimba zili kuno
kukhala m'mudzi muno sitikana
ngati Lawrence chakana
chikwiri mofaya