Intro
Moyo wako ndiwofunika
Kasungu music again
It's black volt
Eh eh eh
Verse 1
Mwana wanga wululu wako
Usiku wukulila wekha m'chipinda
Wukuganiza ngati palibe amakukonda
Wukuganiza kuti imfa ndiyo njila yokhayo
Koma mvetsera nkhani yangayi
Ine ndinakhalapo pomwe iwe ulipo
Ndinaganizapo zomwe iwe wukuganizazo
Koma mulungu anandigwila dzanja
Hook
Wosazidelela moyo wako ndiwofunika
Wosazidelela moyo wako ndiwofunika
Vuto lilonse limatha
Koma moyo wukatha subwelela
Wosazidelela moyo wako ndiwofunika
Wosazidelela m'bale wanga,m'longo wanga
Wosazidelela moyo wako ndiwofunika
Zonsezi zizatha khulupilila one
Manyazi azakhala Kwa adani ako
Wosazidelela Kwa iwe ayi
Verse
Mavuto sichizindikilo kuti ndiwe wolephela ayi
Mavuto ndi sukulu yamulungu
Devidi anamenyana ndi goliyati
Ndipo yosefe m'ndende asanakhale mfumu wuzaziwa chiyani ngati wukupha moyo wako
Wukupha maloto amayi ako
Wukupha ana akanabelekedwa
Wukupha nyimbo yomwe wukanatulutsa
Ndipo adani ako....sazalila
Azangoti walephela...sazachita manyazi ayi
Azakhala ndi nkhani yokuseka koma wukapambana....manyazi azakhala Kwa iwo
Hook
Wosazidelela moyo wako ndiwofunika
Wosazidelela moyo wako ndiwofunika
Vuto lilonse limatha
Koma moyo wukatha subwelela
Wosazidelela moyo wako ndiwofunika
Wosazidelela m'bale wanga,m'longo wanga
Wosazidelela moyo wako ndiwofunika
Zonsezi zizatha khulupilila one
Manyazi azakhala Kwa adani ako
Wosazidelela Kwa iwe ayi
Bridge
Ngati wukumva kulemedwa lero ,choyamba yankhula munthu
Wusakhale wekha wukapsinjika
Pemphera kwamulungu akuvera
Misozi yopanda mawu
Kumbukila dzuwa limatuluka m'mawa wuliwose
Moyo wako ndi buku
Ndipo wusatseke pa mutu wuliwo
Nkhani yabwino yikubwera
Hook
Wosazidelela moyo wako ndiwofunika
Wosazidelela moyo wako ndiwofunika
Vuto lilonse limatha
Koma moyo wukatha subwelela
Wosazidelela moyo wako ndiwofunika
Wosazidelela m'bale wanga,m'longo wanga
Wosazidelela moyo wako ndiwofunika
Zonsezi zizatha khulupilila one
Manyazi azakhala Kwa adani ako
Wosazidelela Kwa iwe ayi
Speaking
Abale anzanga one black volt
Ndikulemba buku lamoyo
Kudzela mnyimbo zanga
Ndipo ngati mukunditsata ndiyekuti mukuziwa mitu yanyimbo zanga
Hook
Wosazidelela moyo wako ndiwofunika
Wosazidelela moyo wako ndiwofunika
Vuto lilonse limatha
Koma moyo wukatha subwelela
Wosazidelela moyo wako ndiwofunika
Wosazidelela m'bale wanga,m'longo wanga
Wosazidelela moyo wako ndiwofunika
Zonsezi zizatha khulupilila one
Manyazi azakhala Kwa adani ako
Wosazidelela Kwa iwe ayi