[Intro]
Thoxy kay Mw
Yeah...
The young ghetto yeah..
[Verse 1]
Zilikuti zoti umkandi konda
Tikamayenda anthu kumati Loza ife
Zilikuti zoti umkandi konda ine
Tikamayenda anthu kumati Loza ife
Wayiwala kale momweti timka kondelana
Wayiwala kale momweti timka mvanilana
Wayiwala kale momweti timka kondelana
Wayiwala kale momweti timka mvanilana
[Chorus]
Koma ndati ndza Bwino Bwino
Ndza Bwino Bwino
Koma ndati ndza Bwino Bwino
Zabwino Bwinoooo!!!!!!!!!
[Bridge]
Koma wayiwala kale
Iwe wayiwala kale momweti timka kondelana
Wayiwala kale momweti timka mvanilana
Wayiwala kale
[Verse 2]
Ndika kumbukira
Iwe Felister ukalakwa umkati sakwiye chikondi ndikumvanaaaa
Nanga Lero bwaaa ndikuwoneka
Yeah!!!