Ranking katswiri
Money hunterz Music
Ooh yeah
Woooo
Ine ndikati ochisaka sachipeza
Adzanga ankaseka ndikamati ndili single
Ine mtima kuwawa ndinakanika kudekha
Sikadza kokha ndi chifukwa ndakupeza
Ukandipasa mtima wako ndikulonjeza suzasweka
Day and night ndikuganiza za iwe
Chimwemwe chokha chokha ndikaganizatu zaiwe
Ndili dziko langa langa
Maganizo apatali ofuna kukutengera
Ndikamati makukonda uzizitengera
You do shine Mamie ndinu pendadzuwa Mamie munakongolesa
Kukongola kwa natural kazi osunga culture
Bwera undisainire undilonjeze olo atabwera Mr money chikondi chathu saza casher
Love is crazy ndazelezeka
Ndikanga kanga Kosafuna zambiri Amangofuna attention salada yanga mbiri
Ndizokuti kalakwisa kaziyu amakambika
Ndimazitenga zapamwamba coz ndizosililika
Forever mine tandimwetulire
Chikondi ndi chambiri bwera ndikupakulire
Chikondi ndi anthu awiri Bwera tichisamalire
Tiye tizikondanabe osayika malire
I don't mind mpaka zakalambe nawe
Olo ati kambe ndizakhalabe nawe
C'mon beib osazitengera, azasiya, akazapeza pothera
Iwe ndi machine kuposera Auto teller
Chibwana changa chonse pa iweyo chinathera
Chikondi chathu chakuya chosawoneka pothera
Zathuzi ndi zeni zeni zosachita kukopera
[Intro]
[Verse]
[Acoustic Guitar Solo]
[Male Vocal]