Intro
Eeeee eh eh
Kasungu music
It's black volt
Hook
Mukufuna chani akazi
Munthu m'modzi amuna gulu
Mukusakatu pofela inu
Abwele wuyo... Kulola
Abwele awo... Kulola
Abwele awa... Kulola
Mukufuna chani akazi
Munthu m'modzi amuna gulu
Mukusakatu pofela inu
Wametewe... Mamuna
Wosasamba... Mamuna
Inu mwati bola ndalama
Verse
Muzaka zam'mbuyomu akazi
Wumati wukawafusila wumadikila
Lelo kusiyana kwake ukafusila pompo pompo
Ziko lino likufuna kusamala
Chikondi sungachivetse
Akanakhala mulungu amawonetselatu mavuto amusogolo
Inu simukanapanga chikondi
Mwina pano muli wosaziwa
Koma mawa lanu ndilowawa
Samalani moyo akazi
Ziko likuthamanga ndipo musalitengele
Tayimani ndinu ilo lizithamanga
Lekani kuchulukidwa azimayi ndi asungwana
Hook
Mukufuna chani akazi
Munthu m'modzi amuna gulu
Mukusakatu pofela inu
Abwele wuyo... Kulola
Abwele awo... Kulola
Abwele awa... Kulola
Mukufuna chani akazi
Munthu m'modzi amuna gulu
Mukusakatu pofela inu
Wametewe... Mamuna
Wosasamba... Mamuna
Inu mwati bola ndalama
Verse
Kuli azimayi ena kukhala ndi wokondeka m'modzi samatha
Iwo koma ambiri kodi mufika nazo patipo izi
Makolo wolangiza analiko koma kusava
Amuna amakomadi koma Iwowa Ali ngati mkuyu
Wopezeka ndi nyelele mkati mwake
Fundo za amuna amafuna kukukopani mawa lino muyipaso
Ena ma anja awo anatha chifukwa, chokhulupilila mamuna wachibwezi
Tawafuseni mavuto womwe anakumana nawo
Nanga lelo amafunaso kugwa muchikondi?
Ili ndi langizo la ine Black volt kuti wosakomedwa
Chikondi chibwela ndipo chimapita
Wochifuna akanabadwa ndipo icho sichingasinthe
Hook
Mukufuna chani akazi
Munthu m'modzi amuna gulu
Mukusakatu pofela inu
Abwele wuyo... Kulola
Abwele awo... Kulola
Abwele awa... Kulola
Mukufuna chani akazi
Munthu m'modzi amuna gulu
Mukusakatu pofela inu
Wametewe... Mamuna
Wosasamba... Mamuna
Inu mwati bola ndalama
Bridge
Inu ndi mchere.... Inuyo akazi
Musasungulumwe.... Inuyo akazi
Chikondi chilipo.... Ndipo chizakhalapo
Wina amafa Wina a amakhala...ichi ndicho chikondi
Lemekezani mtima wanu
Kuti mawa lanu muzalangize ena wubwino wake
Chikondi chinalembedwa ndimulungu
Ndipo azafufuta yekha mulunguyo
Hook
Mukufuna chani akazi
Munthu m'modzi amuna gulu
Mukusakatu pofela inu
Abwele wuyo... Kulola
Abwele awo... Kulola
Abwele awa... Kulola
Mukufuna chani akazi
Munthu m'modzi amuna gulu
Mukusakatu pofela inu
Wametewe... Mamuna
Wosasamba... Mamuna
Inu mwati bola ndalama
It's black volt, Kasungu music, mtema gaye
Hook
Mukufuna chani akazi
Munthu m'modzi amuna gulu
Mukusakatu pofela inu
Abwele wuyo... Kulola
Abwele awo... Kulola
Abwele awa... Kulola
Mukufuna chani akazi
Munthu m'modzi amuna gulu
Mukusakatu pofela inu
Wametewe... Mamuna
Wosasamba... Mamuna
Inu mwati bola ndalama