(Intro)
Iyeee seen,iyeeee ife pano tikumwa,kumwa,kumwela Panganga tchilu sport iiiiiii eeeh
(Hook )
Ife pano tikumwa,kumwa (kumwela pa nganga tchilu sporting )ngat mufuna kumwa, kumwa (bwelani Panganga tchilu sporting )ndikunena kumwa iiiiiiiiii iyeeh
(Instrumental 15 seconds )
(Verse1)
Ife TIKUNVA KUKOMA NDI MOWA,DRINK YA BWINO YALOwa,palibe ntundu wamowa otsowa,SOUND NKATI TILOWAAA, IWE DJ TANGOKWEZA PAN'GONO (3TIMES INSTRUMENTAL JAHMING) CHI VIBES CHILI NKATI ,KU FIRA NGATI MATIMATI,IWE DJ TANGOKWEZA PAN'GONO (3TIMES INSTRUMENTAL JAHMING )
(HOOK )
IFE PANO TIKUMWA, KUMWA (KUMWELA PANGANGA TCHILU SPORTING )NGATI MUFUNA KUMWA,KUMWA (BWELANI PANGANGA TCHILU SPOTTING )NDIKUNENA KUMWA IIIII IYEEEH
(INSTRUMENTAL 15 SECONDS )
(VERSE2)
UKAMACHOKELA KU BORDER KUMULANJE,UNGODUSA PA MULako pamenepo nde kuti nkhawa njee, bayala nthumba mwako eeeh yah nonse ochoka town,pambanani lutchenza NDI chonde mukatelo mupawona,PA orphanage ili nkhonde.nganga TCHILU SPOTTING eeeee. IWE DJ volume taponya (3TIMES instrumental harming )
(Instrumental 15seconds )
(Hook )
Ife pano tikumwa,kumwa (KUMWELA PANGANGA TCHILU SPOTTING )NGATI MUFUNA KUMWA, kumwa (bwelani PA nganga tchilu sporting)NDIKUNENA kumwa iiiii yeeee
(ENDINGS)
IWE DJ volume PANg'ONO(3TIMES instrumental harming ) iiiiiii yeah,kusangala NDI kumwa iiiiiii iyah chokumwa chilichonse MUFUNA HeH HEH INE NDI HENZO D MALAWI HEH HEH MBONI NDI SIMPONZI HEH HEH MALO ake NDI omwewa PA ,PA, PANGAnGA (TCHILU SPORTING.