Together we can as you you know to day is very fantastic,tikadikilira you day Malawi ense kusangalala,kunyadila kuti lero zonse zili m'manja mwathu ndiye tiyipasa moto makolasi tibebesa monga youthday, kusogolo kuli alinafe,constance kuipasa moto bwana Joseph kuzavokera mochitisa chidwi,yayaya abusa timakukondani tili pano chifukwa Cha Inu mulungu akudalitseni,ok ok ok nkhulambe CAs mulungu amatikonda.atsogo amacheso lero dekhani makolasi tibebesa tokha kwinaku bwana Innock akuchapa ng'oma kukhala ngati wayambana ndi MANEB.ajuma anamsongole kuvina mophyesa m'tima Satana wachita manyazi.ooh my god ooh my god.sindingaiwale bwana chair Godfrey mumakwana tili ayouth ochuluka nonsenu mulungu akudalitseni.nkhulambe yuth together we can