Hmm hmm hmm hmmm
I know thawi zina timayambana koma
Maso anga amayang'ana Bola
Ndizikukonda iwe wekha poti
Mtima wanga wavomeleza
Ndeno undikondeeeeee eeeh ehh
Undikonde, undikonde, undikonde hmmm
Sometimes tumakangana koma
Timavesesana anthu mkumatidabwa
Bwanji chomchi timakondana
Ndeno undikonde eeeeeeee eeh eeeh
Undikonde, undikonde, undikonde hmmm
Grace undikonde gile undikonde ooo ah