Mukafuna mfumu yabwino komaso yofikilika ndi a kuluwemba two ndipo ndi mulela khugwa wathu mfumu yotakataka komanso yothamangira anthu ake akagweledwa vuto ndi akuluwemba two ndi mfumu ya mfumu tiyeni tiwalandire komanso kwapasa ulemu
Chorus
A kuluwemba two omwewo kuti wawawa×3