Okondedwa mzanga !
Bwanji osandipatsa danga mai kalanga
Utangochoka tonse unatilanga lero mwana akufuna amama zolakwika ndayesera kunama kumlera ndekha ndayesa za drama
Popanda iweyo sikuphula kathu ndrama
Mesa kod mbalame zofanana mawanga ziulukira limodzi wamusiya mwana wanthu akukhetsa msonzi mmmmh akukhetsa msonzi