|intro |
Plus plus Malawi
Squad squad haipa
Gun de power
|chorus |
Ea koma m tikanati tisakumane Inu ndi ine sizikanayenda munapanga bwino kufunsila ine
||verse |
Real iwe ndine timakondana
Tizabelekelananso ana
Amphavu eya athanana
Girl i love u
And I need you
I don't wanna to leave you