(Intro)
(Wolusa!)
Uuuu yeah yeah
It's on me
Yozi'n
Yozi'n eeeee
(Chorus)
Ngati kumwamba kwavomereza
Iweyo ndiyokhayo thiti yanga
Ndani wina apa angatsutse
Kuti ndiwe wanga
Wanga
Wanga
Kuti ndiwe wanga
Wanga
Wanga
(Verse 1)
Maao anaona
Mtima unasakha
Kuti ndiwe wanga
Kuti ndiwe m'mama eeeee
Mom iwe ine ndi mpaka kale
Zoti zakusiya paliponse izo usamaganize
Amene unasitha mind yanga yonse ndiwe
Ndinakukonda ndinakusakha never leave you away
(Pre chorus)
Mom ndinu one
Special one
Never see you kumbali
You my only one
Zokutaya ayi
Iwe ndine ndi mpaka
(Chorus)
Ngati kumwamba kwavomereza
Iweyo ndiyokhayo thiti yanga
Ndani wina apa angatsutse
Kuti ndiwe wanga
Wanga
Wanga
Kuti ndiwe wanga
Wanga
Wanga
(Verse 2)
Jah pomdipasa iwe anadalisa
Ndulonjeza kalikonse zakupangira
Zokukana pagulu izo sindizachita
Your beauty beib yandibalalisa
Zomwe umandipanga n'chikondi mmmmm umakwanira
Ndizikupasa yonse love
Nanji you're my best lovor
Kwaaaanu my best ine ndizafikako
(Pre chorus)
Mom ndinu one
Special one
Never see you kumbali
You my only one
Zokutaya ayi
Iwe ndine ndi Mpaka
(Chorus)
Ngati kumwamba kwavomereza
Iweyo ndiyokhayo thiti yanga
Ndani wina apa angatsutse
Kuti ndiwe wanga
Wanga
Wanga
Kuti ndiwe wanga
Wanga
Wanga
(Ending chorus)
Ngati kumwamba kwavomereza
Iweyo ndiyokhayo thiti yanga
Ndani wina apa angatsutse
Kuti ndiwe wanga
Wanga
Wanga
Kuti ndiwe wanga
Wanga
Wanga
Uuuuuuu yeah yeah
[Male Vocal]