Intro :zin! Elp-zin mw get 361 music
Chorus
Ife ife tili hard kuno (kuno!)
Iweeeh!.
kwayaka moto kuno!
SiTili Pa easy ndi boys
Boys
tungo panga noise
Verse (1)
Ife tili hard ase
Rudeboys tili mad ase
Sitikugwilika
Tayakiratu ase
Iweee!
Ndife Khutu kumve ase
(Bwanji?)
Ma loza sitikumva ase
Okutha kucheza akufunika kuno abwelee!
Amabodzawo akagwelee (gwele)
Ndipo muwawuze kuti azitolere
It's our time we manage it
And
We don't waste it
Iweeh
east or west
Kuno kuli best
Chorus
Ife ife tili hard kuno (kuno!)
Iweeeh!.
kwayaka moto kuno!
SiTili Pa easy ndi boys
Boys
tungo panga noise
Noise noise
Verse
Tungopanga noise
We move fast
And!
We Run fast
Yasa cheese ras
Utsi ufuke basi
Yoh! tili mu circle yoziwa Kutchira
Tupanga zapano
Sizingakukhuze mphwanga ngati sulipano
Iyi ndi Fact
Fact ndimwano
Koma Maloto akowo ndi nthanoo
Ukufuna beef awo koma sathano
Akamati Beef ndiwe ndimangoseka
Munthu oti kwa amuna anzako ukumangothweka
I got the proof
Proof yeee
Chorus
Ife ife tili hard kuno (kuno!)
Iweeeh!.
kwayaka moto kuno!
SiTili Pa easy ndi boys
Boys
tungo panga noise