eeeeee zinayambika ngati zocheza
pamene ndinakuona iwe tamandani
nditangila iwe anthu ose ananditama
zinalizasiliyasi osati zamatama
umene uliweko ziwa kuti ndimakukonda
ndimakukond mmmm ndikukonda
paiwe ndimanthela zokusiyaaa
iwe ndizosathek chikondi changa
ndichoona paiwe tamandani
uziwe kut kumbukani sazakusiya
sizakusiya sizakusiya
awiri ife tinkhare pakana kare
tikuyenda awiri ngati nkhunda