Ayee Ayee It's Prozima Malawi [chorus] destiny ti shirt printing kudinda zovala mwapamwamba x2. [Verse]paja zakumva kupwetekesa mutu simple way mungobwela nokha muzazionele ife a destiny tea shirt printing timadinda ma plain tea shirt jersey njinga za Moto and many more others chulukechuluke wa njuchi umaloza yomwe yakuluma. [chorus] destiny ti shirts printing kudinda zovala mwapamwamba x2. [Verse] Eeee nditakumana ndi malefula,mandevu komanso man kho ndinawafunsa Kodi ma jersey omwe mwavalawa munalembesa kuti oooo kutiko [volcal]Ku Destiny Tishirt printing your design here come my friends don't fear ooo Kaya ma label a chrome heart,versage, Palm angels ndi Mitanda zonsezo ndi zotheka ndi a destiny Tishirt printing[chorus] destiny Tishirt printing kudinda zovala mwapamwamba x2. Hahaha Destiny printing Tishirt Ndi Fire Moto Moto Likhonyowa Prozima Pa makina Yee Big up to Producer Bossaro Vibes Umakwana yeee.