D-HAMZA again
(Kodi mulibwanji mulibwanji lija ndikale ndinachoka mpaka lero sindibwera ndafuna ndikuwudze ndiwamene wanga mtima unasakha ndikudziwa ndayenda ndipo nawe wandeye koma Mulungu anatiyanjanisa pano ndili ndiwe ndiwendiwe
Beab usalire ulindine beab usalire uli uli uli kulikonse komwe iwe uli ndati usalire sizingatheeeeke kukusiyawekha ndati usalire ulindine uli uli uli
Zachanga chokondi ndinakupasa nawe chilandire chonde usalir I never leave you alone coz your my heart you my everything kukhala opanda iwe ndili ngati mtengo opanda midzu come to me that's why am singing no time to my ex chifukwa nakudalira opanda iwe ine ndalira
eab usalire ulindine beab usalire uli uli uli kulikonse komwe iwe uli ndati usalire sizingatheeeeke kukusiyawekha ndati usalire ulindine uli uli uli