Akanaziwandani time yathu izakwana inaliyopweteka koma pano ikukoma zakare tsiziiwarika eya tiyetiziware ndimene moyo umakhalila nanny
Nakha bwanji ukukumbukabe zakare kukumbukaabe poti tayenda muzotan
Komabe ziiware ziiwareeebe
Ukuyenela uzikonkhwa usamanganizire kwambiri
Pazana ndinali pasi pano
Tili pa mphiri zokhumba zanthu
Zinali zambiri poti zizayendaa
Mmmmmm kay you