Intro
Yeah
It's Dick T
Nafeso timvekeko
Verse 1
Kupanda kukuona babe ndimadwala
Ndikakhala nawe mavuto ndimaiwala
Ndiwe okongola iweyo ndiwowala
Hun ndisaname za iwe ndimasamala
ndiwe chimwemwe changa tamvera
Tandigwile mkono my babe tabwela
Kodi uli kuti simene ine ndakusowela
Zomangokuwonawona ndinazolowela
Ukazandisiya my babe ndizalowelela
Ndikakhala ine nde simzakusiya yiwala
anayesesa mbili kuyidesa Pano yiwala
Akapasule ali mmadzi eya akunamaa
Chorus
Chisankho changa zokonda zanga
Mmmmmm ndiweyo babe
Ine ndasankha ndakonda iwe
Tamvera my babe
Ndikamati ndimakukonda
sikuti ndikungonena oh yeah
Udziwe ndimakukonda ndimtima onse
Oh yeeeeee! babe oh yeaeeeee
Ndimawerengera iwe iwe iwe
ndimadalira iwe iwe iwe
Chisankho changa ndiwe ndiwe ndiwe
Verse 2
Mwina sumadziwa chomwe ndimakukondela
Eya sumadziwa Mene ine ndimamvera
Unasintha Khalidwe langa iweyo utangobwela
Chibwana ndinasiya za iwe ndinavomela
Umandikwanila sindimafunaso Wina
Dziwa mtima wanga ndiweyo unawina
Ndikufuna mayi wa ana anga uzakhale
Za iweyo abale ineyo ndinawawuza kale
First born walusungu, winayo ndiwakisa
Kuthokoza mulungu pamene watifikisa
Ona adani onse manyazi wawachitisa
Amkadwala nsanje aja Pano awachilisa
Yeah umandifilisa, good life umandifilisa
Tamyo
Chorus
Outro
Ukamakhala uzidziwa kuti
Dick T za iwe amasamala
Ndipo amakukonda