Prompt / Lyrics
Zamuntima ndizawekha Koma ine ndikuuza
I'm really serious with you sindikufuna Kuku yuza
Ndikufuna zeni Zeni osati zamasewela
Chikondi cha mpaka kale infa ndiyo pothela
Ndayenela wabanja osati chibwezi chabe ayiii
Munthune ndikukula sinkubwelela kuumwana ayiii
Nde tisananyamuke ulendowu ndikufuna undiuze
Ulinane serious kapena ungofuna undiyuze
Chorus
Sindikufuna kupanga mistake yomwe ndinapangapo ndi Wina
Ngati sunakonzeke ndiuziletu nkapeze Wina
Sindikufuna kuzalila wanditayisa nthawi chabeee ndechilungamo tandiuza zinthuzi tisanaziyambe

Ndiye tandinvela
Khutulo tatchela
Ulendo tayambau siophweka
Eya love is sweet
Koma zikhomoso zimapezeka
Ansanje ndi mijedo osalephela
Otikonda alimoso nsanja azatimangila
Koma chachikulu ndikunvana kwathu
Akabwela ndi nkhani zawo nvela Koma usatolepo kanthu
Tikagwa m'mavuto tililile Kwa mulungu wathu
Chorus
Sindikufuna kupanga mistake yomwe ndinapangapo ndi Wina
Ngati sunakonzeke ndiuziletu nkapeze Wina
Sindikufuna kuzalila wanditayisa nthawi chabeee ndechilungamo tandiuza zinthuzi tisanaziyambe
Sindikufuna kupanga mistake yomwe ndinapangapo ndi Wina
Ngati sunakonzeke ndiuziletu nkapeze Wina
Sindikufuna kuzalila wanditayisa nthawi chabeee ndechilungamo tandiuza zinthuzi tisanaziyambe
Ziwadintima wanga wakondaiwe
Wakanda iweeeeee
Chikondichanga chonse chili paiwe
Chilipaiweeeee
Ngati tili limozi ndigwile zanjaaa
Ulendo tayamba sizosiyana kusemphana njila
Iwe ndiine ukunenesa mpakana m'mandaaa
Chorus
Sindikufuna kupanga mistake yomwe ndinapangapo ndi Wina
Ngati sunakonzeke ndiuziletu nkapeze Wina
Sindikufuna kuzalila wanditayisa nthawi chabeee ndechilungamo tandiuza zinthuzi tisanaziyambe
Sindikufuna kupanga mistake yomwe ndinapangapo ndi Wina
Ngati sunakonzeke ndiuziletu nkapeze Wina
Sindikufuna kuzalila wanditayisa nthawi chabeee ndechilungamo tandiuza zinthuzi tisanaziyambeTags
Dreamy Acoustic Ballad with Soft Guitar and Whispered Vocals
4:59
No
3/21/2026