Chikondi sagawan ngat ndiwo beib ndikupereka zanga zonse kwa Iwo
Chikondi sagawan ngat ndiwo beib ndikupereka zanga zonse kwa Iwo
Izi pangu izi pangu zimakupangitsa kubalalika mamuna muchikondi amalalika
Mkazi amavetsera
uku khutu atatchera
Inde amawoneka ngati opepera
Izi nkhani Zina
Chikondi sagawan ngat ndiwo beib
Ndikupereka zanga zonse kwa Iwo
Chikondi sagawan ngat ndiwo beib
Ndikupereka zanga zonse kwa Iwo
Ndikati ndiwonetsetse ndikungofuna undikondetsetse beib usanditalikire undiyandikire
Mtima wanga uli nawe
Beib uzakhala nane
Ndiwe wekha
Uzandisamalila
Sizalola uzizalila
Chikondi sagawan ngat ndiwo beib
Ndikupereka zanga zonse kwa Iwo
Chikondi sagawan ngat ndiwo beib
Ndikupereka zanga zonse kwa Iwo
kugwa chikondi dzikolina kumakupangitsa
Kusintha Zina
Chikondi sagawan ngat ndiwo beib
Ndikupereka zanga zonse kwa Iwo
Chikondi sagawan ngat ndiwo beib
Ndikupereka zanga zonse kwa Iwo
M Jay p145 mw
Good boy