Intro
Mmm yeah
Kasungu music
It's black volt
Hook
Ena Amati ndine big man
Ena Amati sindine munthu wamba
Kodi ndine ndani
Ndine ndani ,ineyo ndine ndan
Verse
Kuchokela umwana kufikana kukula
Ndakhalapo dolo ine nthawi zonsezi
Ena ankaphweketsa ukuku
Koma Kwa anthu ena ine ndinali dolo
Koma Pano ndafikapo udolo uja wachuluka
Ndeno ndikudzifusa ine fuso langa Bali
Hook
Ena Amati ndine big man
Ena Amati sindine munthu wamba
Kodi ndine ndani
Ndine ndani ineyo, ndine ndani
Verse
Udolo ndowonse wangawu ndikakawa
Eti kulemba nyimba anthu mpaka kugoma
Eshi ndine ndani ineyo ndine ndani
Pali inepa eti mpaka kuveka ,or ophweketsayo ayambila pati
Palibe kufoka paja lusoli ndilathu
Kafuse kukasungu anthu akundiziwa
Kafuse kambulile anthu anthu akundimanya
Ndisaname apa lusoli linali ready
Hook
Ena Amati ndine big man
Ena Amati sindine munthu wamba
Kodi ndine ndani
Ndine ndani,ineyo ndine ndani