Yankho scheme yabwera kuzathetsa mavuto akusowa kwachakudya ndi njala
Ulimi umafuna kukhala pamodzi.
Osadzimva undekha tiyeni tiyende limodzi
Anthu awiri amapanga mudzi.
Ulimi othilira umafuna madzi
Zitsime tiyeni tikumbe limodzi.
Zonse zikufuna umodzi
Yankho scheme yabwera kuzathetsa njala ndi mavuto akusowa kwandalama.
Amabungwe ndi aboma bwerani tili ndizambiri zosowa.
Tigwireni manja tikufuna zitsime zakuya komanso ma engine asola amakono
Malawi 2063 vision timukwanitsa popanda tsatsa paja amadalitsa opatsa .
Yankho scheme yabwera kuzathetsa njala ndi mavuto akusowa kwandalama.
Timapezekera kwanankumba group nankumba m'mudzi mwa ngundende
Ngat simunagure katungu Monga tomato, dowe, nyemba, bonongwe, mabilinganya ndi zina zakudimba mukuchedwa.