Maijaz
Iwe ndinkaz amene ine ndamukonda wekha ukuziwa sinzakuyenda njomba!!
Koma anzako anzako anzako ayiweyo amakunamiza cholinga choti undisiye honey koma wekha ukuziwa mene ine ndimakukondela wekha ukuziwa zachikondichanga iweyo!!!
Beiby Ndimakukonda ndi makulava!!
Chonde usapite!!
Beiby Ndimakukonda ndi makulava!!
Chode usandisiyeso.