Sakha chimozi sakha iweeee
Sakha chimozi sakha chimozi
Sakha chimozi sakha iweeee
sakha chimozi sakha chimozi
Ichichakoma aaa
Ichichakoma ichichakoma uzagwanacho
Kutumikila yehovahhhaa aa
Sakha chimozi sakha chimozi
Kuzicha achristu koma kumwamowa sikulekaaa
Sakha chimozi sakha chimozi
Ati ndi abusa koma akazi thathathaaa
Sakha chimozi sakha chimozi
Ohoo langa ndifuso
Uzifuseeiweehhe uzifuse iwe
Ukafikila
Ukafikila kuti iweukazafa