Sindi sitha zina paja ndimakhalabe zggy
Mistake imozi umatha kulira moyo onse
Eti panopa ndukanika kunena am sory
Zoona ine kukutaya pamene ndinali nawe
(Hook)
Komano ndazindikira (chibwanadi chimalanga nga nga)
Panopa ndazindikira (opusa chibwana chilanda nda nda)
(Verse 1)
First of all ndinene kuti am sory
Kungoti ineyo i dont deserve to be alone
Komano chibwana changa chandifikisa pa chonchi
Pali zambili zokamba komano ndingofikira pa plot
Unali wanga ndinali wako timkakondanananana
Mavuto chotani sunkandisiya unali nga nga nga nga
Poti pali awili sizilephera tinkayambana na na
But one thing tinkaziwa kuti ili ndi banja nja nja
Koma mutu umozi susenza denga ndakhulupilira apapa
Ndimafuna kukonza zithu munjira yanga yanga
Ndinaiwala kuti choipa sakonzeraso choipa anganga
Ineyo sindinasithe mpaka kufikira kundisiya amama
Oooooh pano ndikumvesano chisoni
Ana abalalikana apa akusowa chathu chikondi
Ndikanaziwa kuti izi zizathera chonchi
Ndikanakugwirisisa olo nawe uli ndima fault
(Verse 2)
Ngakhale olo ndayakhula ndikuzwa sizisitha
Poti muthu ukabadwa kumasala ndikufa
Inde mtengo ukagwa kumasala ndikuuma
Nyimboyi ndangoimva ndicholinga choti ungoziwa
(Panopa ndavomereza kuti mamie ndakusowaaadiii)×2
Panopa ndatha ma planiiii
Sindikuziwa kuti zindithera bwanji
Tikakhala limozi zochita zako zimandikwana
Komano ukasuthapo mpameneso ndimakusowa
Kaya unandipanga chani apa pokha moyo ukubowa
Ee nyamata wanga ndamusowa
Kodi msikana wako sumusowa?
Sikuti tibwererane ndangofuna ungoziwa
Sinanga maligileti achuluka awa achulukaa wa achuluka awa)×2