Usadandaule mani iii usalile.
Pamene nyengo zako zavuta.
Moyo wako ndimene umayamba kusutha.
Usagonjere ai koma ponya ino.
Thawi zonse khara olimbika.
Tsogoza yawe patsogolo.
Poti lathu lalikulu kholo.
Usamadandaule pamene
Azako akunyoza.
Koma apephelele kuwafunira zabwino.
Ngat mene anachitira yobu.
(Pri-corous)
(Poti yawe ndiwodabwitsa.)
(Madalitso ambiri amavumbitsa.)
Poti yawe amatingonda.
Ndie sangalole kuti uvutike.
(Chorus)