(Hook)
Mmm mani dii afana
Its tommy lee
(Verse1)
Ea iwe beib unanichita chipongwe
Ine oakut nilo nomo chifukwa chakuti
Chilichose chomwe iwe umapanga ine ndimangoziona
Pakit sinimadziwa chobwela mawa
Koma ap ndapeza wina emwe ndikudalila kuposa u
Akazi owadziwa madzi osat ngai iwe
Ponya dowe apa ndikapita amapeleka
Chilichose ndimafuna kma sikuti ndi hule ayi
Koma kuonesa chikondi kwamuna ake
The name is chalite
Ndamene ndikukhalila moyo panopa oyeh oyee eee
(Hoo)
Iwe beib ndinasangalala pachipongwe chako
Pakut chobwela mawa sichidziwika
Ine ndimangokhalilamo osadziwa chimene iwe ukuganiza
Pano nakhulupilila kuti muntima mwa mzako ndi mnthumbas
Sinimakhlupilila sindkhulupilila ooo yeee
Mmmm mmm mmm
(Verse2)
Ndinaiwala munthu m'modzi lelia
Eadi zedi amandikondadi
Koma paja amati osamatengeka
Ni vula yachiwawa
Chifukwa chakuti sikhalisa
Anavela zokamba azake
Zinapweteketsa
Umusiya mavuto
Tikunena pano alibeso olokono
Chibwezi amaesa ngat amene akumamupangila
Nae sapangaso zibwwzizo
Koma osamathamangila kumeza
Chinthu chikanakoma
Pano ukubwela ukufuna reback
Never give u another chance
Unanitenga opanda pake
Pano ndine tomuzi tchalite oye
Mmmm mmm mm tchalite
(Outer)
Oooye mmm
Mmm
Mmm ine ndi toma aaa
(Ending )
Fillodi studioz
Its pepseen on the truck
Onite