[Intro]
Mmmm may say sang froid mm mm
[Verse 1]
Hello Alice, ndwe perfect girl and I love you
Ndifuna ndizikuwona everyday mm mm
Watenga malo mumtima mwanga Alice
Wena akufuna iwe basi beib be with me
My feelings ndikumafuna iwe basi mmm
You're so beautiful and pretty, Alice mm mm
Wena fecuz akufuna iwe, Alice
[Chorus]
Dear God, please open the eyes for Alice oooooo
Muoneselen kuti ndi chimwemwe changa oooo
Ndimamukonda!!!! Ndikhale soja wake, mteteze wake
Oooooo beautiful girl mm mm ooooo I love you, being
[Verse 2]
Ndatopa ndikukhala ndekha ine
Ndatopa ndikudikirila iwe, makware akufuna ave kuti ndiwa ine, iwe
Better love ndikupasa iwe, trust me ndikukonda ine ooooo
Ndikuziwa kuti ambinji amafuna iwe, koma ine ndakondaso iwe
Ndizikuwona iwe, ndikulota ine, ndizikuganizira iwe, beib ine mmmmm