(chorus)
Sikuchenjera Kwanga no
Kapena nzeru zanga noo
Koma chisomooo chisomo moo
Chisomo Cha Namalenga
(Verse 1)
ndadzuka mamawa ine ndili ndi thanzi lonse
Opanda nkhawa, osasowa kalikonse ne
Zonsezi ndichauta ndiye wandifuka tila
Palibe sowina yemwe nditsa tila
Anga ndimatamando
Kwa iye wamwambamo
(chorus)
Sikuchenjera Kwanga no
Kapena nzeru zanga noo
Koma chisomooo chisomo moo
Chisomo Cha namalenga
(Verse 2)
Ngat ukuyenda ziiwa kuli namalenga
Poti ena alichigonele muchipatala
Mpaka kutukwana kumwamba pot wasowa ya mbatata?
Gwada kwa namalenga iye akupatsa bata
Mavuto akadza ndimatulila iyeee
Musaone kusangalala akundisamala mbuyee
(chorus)
Sikuchenjera Kwanga no
Kapena nzeru zanga noo
Koma chisomooo chisomo moo
Chisomo Cha namalenga
(Outro bridge)
Yahwe la ndi la ni ule muuu (ulemu)
Poti pa libe chimalaka inuuu (inuuuu baba)
Yahwe la ndi la ni ule muuu (ULEMU)
Poti pa libe chimalaka INUUU (MULUNGU! WANGAA!!)