Nkhani ya moyo wanga........ tsiku lina muchaka Cha twenty nineteen oohh .... twenty nineteen......ndinati ndiyendeko eeeeeeeee Mamane ndili nkati moyenda ndafka kwayasenya .......ndinaona nyenyezi kutsogolo kwanga ndinadziwa kut ooh ...ohhh iyi nd nthiti yanga ..... nthiti yanga esnart....my love.... esnart my love
Mphatso pomwe anakonda esnart Nalibe kalikose koma ndinadzwa kut uyu yekha ndiwanga ......oh my love my eeesss my lover......atandilora ulendo wachikondi unayambika......eeeeeyaaa tinauyamba ulendo
Tinadutsa muzambiri amayi zambiri mphatso ndi esnart apilira muzambiri limodz.......takumana ndizowawa zambiri pena tinkaona ngat tathera pompo.....koma pot kumwamba akalemba alemba ......oh palibe angatsutse ........amake wit anali mbali yathu ......oohh asisi ma wit ankatilimbikitsa ....... esnart anapita kunkhamenya kusekondale ndipo ndinamudikra mpaka zaka zonse zinai ......eya zaka zinayi ....Ali kusukulu nkaz wanga okondedwa
Mula wanga ndinu dolo katatu......Mula ndinu dolo kwambiri ,munkandilimbikitsa ndikamafooka .....kundphunzitsa kulimba mtima oh bambo a witi ....... ambiri ankatiseka koma lero akululutira tskuli lija ndilero vina nkaz wanga okondedwa.....vina mama
Es ndwe chisankho changa......ndipo iweyo ndwe zanga wamoyo onse .....eya nzanga ....oh lero anthu akutidziwa chifukwa Cha kudalirana kwathu .....poti zinayamba mwachibwana koma lero ona pomwe tafika .......