Yo major gangster Mwa S tigo Malawi spolith government pripizenting sorry Dali thing mwana wa gele
Wa masiye akubadwa dziko La pamsi, Gakhale ukusowa ma silipasi, Koma yehova usamuyang'anile pansi, Usiku ndi usana ungokhalila nkhwani, Azanganu Santana anakunamizani, Chifukwa nabwla kuti nikuuze nkhani, Kuti ukapepha ambuye amapatsa ambuye amapatsaaa
Ukapepha ambuye amapatsa, tangodekha mtima wako uzikhala wofatsa, Yesu salephela amakwanilitsa .
Ukapepha ambuye amapatsa, Anzanu anapenpha anapeza ma mapasa inu pamene mutangokhala inu Pomona mayesa zayenda mumankhwala, Koma Anzanu amavutika ku sala inu kumati amisalaaaa, mulungu azabwela ngati mbala, Azawapeza ena ali muma bala, Chitsazo mutengele make mike, Anawaptsa Salome komaso Mike, Sanadelele koma kuyamika kwa Jaaa, mesa ukapepha ambuye amapatsa, Dzina lamulungu muliyike patsogolo nthawi Ina, Azakuchotsa mukapolo ndipo, Naweso uzasangalala, Mavuto ako Ose kodi mesa uzaiwala
Ukapepha ambuye amapatsa, tangodekha mtima wako uzikhala wofatsa, Yesu salephela amakwanilitsa
(Ambuye amapatsa ambuye amapatsa, Owooo Owooo, Ungoyika Dzina lake pa tsogolooo, dzana lake patsogolooo Azakuchotsa mukapoloooo) Mike mwana wa Gele,...................................................