Ambuye munava kulila kwanga
Mwandichosa muukapolo
On this earth you made my life feel better
Thus why i choose
Koma atate kusakha imwe ine ndalondola
Kuyenda ndinu ine ndikondwela
Here my song to you
Iiinee ndasankhaaa
Iiinee ndasankhaaa imweee
Ooh ndasankhaaa
Iiineee ndasankha imweee the great God
Dziko ili zokhumba zambili
Koma zikomo pochosa chikhumbokhumbo
Kadakhala nd an chipanda inuyo you might king
Kuyenda nanu ine ndkondwera
Kukhara nanu ndikhumbenge
Koma ndasankhaaa
Iiiinee ndasankhaaa
Ooh ndasakha imweee
Ndasakha I'm we yaweh