My mama sent me off early in the day
Ndikagule sugar ine ndisachedwe
Walking so slow tulo in my head
Gangster anauyamba ulendo sanaphwekese
After 2 minutes ndinadzitolera
Tulo tonse tija tinabalalika
Gangster mood on kuyenda mozipopa
Chest pamtunda eni ghetto azioneka
Ndi sugar ndinatumidwa, koma mtima wandigula
Ndinangomuona, dziko lonse linaleka kuyenda
Ndinkafuna kuyankhula koma mawu anandithawa
Girl, iwe ndi delilah, wandigwira mtima wanga
Ndikudusa chapamtunda down the road
Ndinaona kuwala like an engel
I was stunned she was so beautiful
Koma ine nditangomuona aaaaaa
Amama malephera kuyenda ooooyeahh
Anali akusesa koma thupi lake zomwelimapanga
Amaaaama amaaaama maa
Mtimawu unayamba kuthamanga
Nawo mabondo ankanjenjemera
Zoti makagula sugar naiwala
Ndi delirah chomwe Samson anafela
Ndi sugar ndinatumidwa, koma mtima wandigula
Ndinangomuona, dziko lonse linaleka kuyenda
Ndinkafuna kuyankhula koma mawu anandithawa
Girl, iwe ndi delilah, wandigwira mtima wanga
I was like damn ndimuyankhule
I want to say hi mawu sanatuluke
Mtima umkagunda ngat drum yamchurch
She just smiled ngat amadziwa zonse
Ndinayesa kukhala taugh kuima mwa straight
Koma myiendo inali pa jelly state
Ndi sugar ndinatumidwa, koma mtima wandigula
Ndinangomuona, dziko lonse linaleka kuyenda
Ndinkafuna kuyankhula koma mawu anandithawa
Girl, iwe ndi delilah, wandigwira mtima wanga
[Male Vocal]