Namadingo
Kondabe Lyrics
Na Na Na Na Na Naaa
Namadingo....
Ine Ku Church Am Just A Member
Ndine Chabe Member...
Member Wamba
Pena NdimaPita, Pena NdimaJomba
Ntchito Zanga Zinazi Kutalitali Ndi Malemba
Ine Ndimangochita Mongozemba Aah
Okondwedwa Bledren, Let Me Tell The Treuth
Ndine Badman LongTime, MøYø Wa Mazuzo Nanga Ntani
[Høø]
KOMA CHAUTA AMANDIKONDABE EEH, kondabee
MWACHISOMO AMANDISUNGABE EEH, sungabee
KOMA CHAUTA AMANDIKONDABE EEH, kondabee
MWACHISOMO AMANDISUNGABE EEH, sungabe
Eeh Eeh Eeh, Eeh Eeh Eeh, Eeh Eeh Eeh
Amandikondabe
Eeh Eeh Eeh, Eeh Eeh Eeh, Eeh Eeh Eeh
Amandisungabe
[vērsē]
Ndivomere Ndine Ochimwa, Iam A Sinner
I Try My Level Best, Koma Pena Zimathina
Sikuti Ndikufuna Ayi, Koma Mavuto NdiOsakamba
January To Dec. Satana Sakucheza Aponya Ma Bomba
Iye Iye, Ndikamayenda Amatchera Khwekhwe
[amatcheta khwekhwe]
Akandikora Ena Andiseke
[Ena Andiseke]
Koma Koma, Koma Koma
Pansi Pa Ntima, Ndimaziwa
[RepHook]
#the_lyrics_music