your boy ishmael, kumalawi kulizisankho tiyeni tikavote mwanzeru, ku chitipa karonga rumphi mzimba tiyeni tikavote, nkhatabay kasungu nkhotakota salima mchinji lilongwe tiyeni tikavote tonse komaso dedza ncheu balaka machinga monkeys bay zomba phalombe mwanza neno tiyeni tikavote , kwinaku blantyre to nsanje tiyeni tikavote mwanzeru.