Vesha malawi my wife is saciah malawi
Tikamayenda limodzi like ngumbi
Situkulekana mpaka kumwamba ndithudi
Sizachilendo kutiona PA Pic
MA hater onse athilidwA palafini
Love yomwe amandipasa
Ndimakanika kuyakhula course ndili ofasa
Tikamacheza no offside nkana ndimatasa
No pay tax uyu ndiwanga km saciah
Ndilekeranji kuyamima Ine
Raffi Eli first borne like eli