Aseee gangah [komweko!!!]
Mmmmmmmmmm
........... Mmmmmmmmmm..... (Give meee your heart........)
Tikaaamayenda gati mapasa
I feel happy ndi la love umandipasa
Seeekerera iwee ndi santa
Ukafunaa money ndilolera ku hasaa tandipase mwayi inee ndi hussler Hesi gangah me name love yako gati ana dzaiphanga aaaaa
Ukandiona ndikuseka Mami ndiwee
Ukandiona ndikumwetulila eya ndiwee
Usadzachokeee udzatenga chimwemwe
Unazikika mu ntimaa mwainee (eeee)
You are the one Mami
(You are the one)
Usadzachokeee udzatenga chimwemwe unazikika mu mtima mwainee (aaaaaa)
Tandipase mwayi(eeee)
Ineee ndikuwine(eeee)
Usanakane tandiyan'ganee give me chance
Sitigazadane ine si Third T kapena Fulositayili tiye tikondane love ya awilii aàaa
Ukandiona ndikuseka Mami ndiwee
Ukandiona ndikumwetulila eya ndiwee
Usadzachokeee udzatenga chimwemwe
Unazikika mu ntimaa mwainee (eeee)
You are the one Mami
(You are the one)
Usadzachokeee udzatenga chimwemwe unazikika mu mtima mwainee (aaaaaa)
[It's boy boy gangah aaaaaaaaa AA]