Allelluya ameeen amen×2
Verse
Ndamupeza mkazi oopa Mulungu
Woleledwa bwino wachikhalidwe
Lero ndilo tsiku lachipangano
Anthu onsewa abwelera ife
Mkazi wanga Talandira sainira
Makolo ako ali pano uchitira umboni
Ndaima pano kulengeza
Kuti ndampeza kuti ndampezaaaa!!
Chorus
Ndamupeza
Ameeen amen mkazi wanga
Amen amen amen×2
Allelluya
Ameeen amen
Allelluya
Amen amen amen ×2
Verse
Ndikutenge kwanu kwa ng'ombe upite kudowa
Akakudziwe anthu kuti ndakonda iwe
Ndiyamike Mulungu chifukwa cha iwe
Wakhala thandizo pa ukwati wathu
Zovuta zinalipo koma watipambanitsa
Lero ndi tsiku lako Talandira sekelera
Talandira Talandira Talandiraaaa!
Chorus
Ndamupeza
Ameeen amen mkazi wanga
Amen amen amen×2
Hallelujah
Ameeen amen
Hallelujah
Amen amen amen×2
Verse
Momomomo
Momoooo momo
Momomomo
Momo momo momo×2
Chorus
Ndamupeza
Ameeen amen
Mkazi wanga
Amen amen amen ×2
Hallelujah
Ameeen amen
Hallelujah
Amen amen amen
Amen amen amen amen amen amen
End
Tiye kudowa aaaa
Talandira tiye eee tiyeeeee.