[Intro]
Rarger b entertainment
"KUMENEULIKO
oh!!!! eyeee'!!!
KUMENEULIKO
[Verse]
hello mwana ndinemayi wako ndava kuti zikukuthekela mwanawe chonde udzitionako kumbukira momwe unatisiyira ndi mmene pano tilili mwanawe or kanganyase kokha lero taponya mwana. indetikuziwa kuti sukondwa ndi zomwe tinene pano koma dziwa kutikudandaula kwakholopalibe kwaiwe chingaende koma mawu anga ndi
[Chorus]
mwananga mwananga mwananga kumeneuliko ndikoyenda mwananga kumbukira komwe unachokera ndikoenda mwananga kumbukira mmene unatisiyira kuyenda mwananga
[Verse]
akuti mpaka mwakwatira koko chinachilichose ulinacho. pogona ponukhira elemelero xovala zako umagula Bello pomwe ine kuno kuchita kusawa salu mwananga chonde tamaganizako ukufunakunyozesa makolo ako zafika potikuyenda pasewu anthu akumalozelana. kukhala ngati wamisala koma tava. izi
[Pre Chorus]
mwananga mwananga mwananga kumeneuliko ndi koyenda mwananga kumbukira komwe unachokera ndikoyenda mwananga kumbukira mmene unatisiyira ndikoyenda"
[Female Vocal]
[Pre-Intro]
D hamza pond mic
Rarger _B entertainment
I represent Sanya gettle bway
[Female Vocal]