[verse]
Ndaziona ndipo ndazigwira
Ndinayesetsa komanso ndapirira
Ndili opanda kanthu, iwe unali nane
Pano nyengo zanga zili beta
Ndi nthawi yabwino kuti tikondane
Iwe ndi ine..
[Chorus]
Inde abale....
Ndapirira, ndapirira ndipo ndapi..
Ndapirira, ndapirira
Ine ndapirira, ndapirira ndipo ndapi..
Abale zoona ine ndapirira
[verse]
Ndaziona ndipo ndazigwira
Ndinayesetsa komanso ndapirira
Ndili opanda kanthu, iwe unali nane
Pano nyengo zanga zili beta
Ndi nthawi yabwino kuti tikondane
Iwe ndi ine..
[Chorus]