It's
Seeeedraaah Malawiii
96 fadah
Verse 1
°I miss friends from zomba
°Kukusowani inu ngini sikufwamba
°Ndamusowa Dhikheziii, Umari kapitoo
°Osatiyendera magaye mulikutikoo?
°Ndamusowa chapotera, Wilfred Martin
°Kucheza amatha, adawa anali machine
°Chaxy kulilongwe, osaiwala gover
°Anali madolo okomesatu macheza
°Wizzy mfana wa bhabha shop
°Ntchana wama beb, ochulukidwa ndima hop
°Achina Simiii ndazimzawo, Prince pa Songani
°Major ndima friends ooonse ndakusowani
Chorus
Ndawasowa azimzanga,omwe ndimkacheza nawo tili pa geri
Ndawasowa azinzanga,omwe tinkathawa limodzi pa gate
Ndakusowa ma frends
Ndakusowani x3
Ndakusowani ma Gayee
Ndakusowani x3
Verse 2
°Achina Nyanga ndilinawo komkunowa
°Andikwana kufika mpaka pondibhowa
°Ndamusowa Sayoo, Mashoo ndi Chimzy
°Kumusi kunasiya kukoma popanda inuyo eti
°Jonzi ikulanga ikutenga anthu ambiri men
°Mwina ikufuna anthu akwane million
°Ndakusowani nonse amene muli jonzi
°Achina jester ndiazimzanu
°Akusowani aziphwanu
°Ndikale munachoka tamakumbukani kwanu
°Kapena tidikile tizakumane komweko
°Ndi azimzathu achima Farack kamwendo
°Tizakumana, Jonz, cape town mwina Dereben
°Osadandaula tizatchira zeni zenii