Chorus
Oooooh uwoooo eee lapa bale wanga lapaiweeee lapa iwe. Kuti ukapeze moyo osatha lapa iweeee. Lapa iwe. Lapa bale wanga lapa iweeee. Lapa iweee kuti ukapeze moyo osatha lapa
Verse
Tayang'ana komwe wachokela taona zambili moyowako wadutsamooo mantha sakukugwila bwaaa walimba mtima choncho bwaaa wayesako kusuta kumwa ndi. Ma hule wachita nawo. Koma palibe wapindula. Nanga bwanji osayesako Zina tatembenuka yang'ana mwamba uwone ulemelelo wa mbuye wafika ndeno talapa zadziko taleka tiye titsamile kwa yehova poti iye nde mpulumutsi wathu
Chorus
Oooooh uwoooo eee lapa bale wanga lapaiweeee lapa iwe. Kuti ukapeze moyo osatha lapa iweeee. Lapa iwe. Lapa bale wanga lapa iweeee. Lapa iweee kuti ukapeze moyo osatha lapa
Verse 2
Wakuuza kale ikenga. Nawoso abusa sakutopa kuthoka za wamwambayo ndeno ukudikila chani taona bad man. Vashico. Ndasitha ndinali wake wa satanayo koma lelo ndazindikila kuti. Dziko ndilonyenga kwake kwa satana ndi kuba kupha. Ndi. Kuwononga pano machimo ndalapa. Zadziko ndataya. Wanga. Mtanda ndaseza. Kutsata mapazi. A ondilengayo ukufuna ine. Vashico. Nda ngelo. Hossana. Tikayimbemwambaaa koma ngati ukufuna kuita nawo mzanga. Ikenga. Lapa ndukuuza lapa ngati ufuna moyo osatha lapaaaa mmm
Chorus
Oooooh uwoooo eee lapa bale wanga lapaiweeee lapa iwe. Kuti ukapeze moyo osatha lapa iweeee. Lapa iwe. Lapa bale wanga lapa iweeee. Lapa iweee kuti ukapeze moyo osatha lapa
Intro
Ikenga. Ft. Vashico this is. Remixxxxx thank you God for the life you give. Amen